Yoswa 15:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Otiniyeli+ mwana wa Kenazi,+ m’bale wake wa Kalebe, analanda mzindawo. Chotero Kalebe anam’patsa Akisa,+ mwana wake, kuti akhale mkazi wake. Oweruza 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndipo ana a Isiraeli anayamba kufuulira Yehova kuti awathandize.+ Pamenepo Yehova anapereka mpulumutsi+ wa ana a Isiraeli kuti awapulumutse. Ameneyu anali Otiniyeli,+ mwana wamwamuna wa Kenazi,+ mng’ono wake wa Kalebe.+
17 Otiniyeli+ mwana wa Kenazi,+ m’bale wake wa Kalebe, analanda mzindawo. Chotero Kalebe anam’patsa Akisa,+ mwana wake, kuti akhale mkazi wake.
9 Ndipo ana a Isiraeli anayamba kufuulira Yehova kuti awathandize.+ Pamenepo Yehova anapereka mpulumutsi+ wa ana a Isiraeli kuti awapulumutse. Ameneyu anali Otiniyeli,+ mwana wamwamuna wa Kenazi,+ mng’ono wake wa Kalebe.+