Yoswa 15:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Otiniyeli+ mwana wa Kenazi,+ mʼbale wake wa Kalebe, analanda mzindawo. Choncho Kalebe anamʼpatsa Akisa,+ mwana wake, kuti akhale mkazi wake.
17 Otiniyeli+ mwana wa Kenazi,+ mʼbale wake wa Kalebe, analanda mzindawo. Choncho Kalebe anamʼpatsa Akisa,+ mwana wake, kuti akhale mkazi wake.