Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 15:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Kenako Kalebe anati: “Aliyense amene agonjetse mzinda wa Kiriyati-seferi n’kuulanda, ndithu ndim’patsa mwana wanga Akisa,+ kuti akhale mkazi wake.”

  • 1 Samueli 14:49
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 49 Ana aamuna a Sauli anali Yonatani,+ Isivi ndi Malikisuwa.+ Ndipo mayina a ana ake awiri aakazi ndi awa: Woyamba kubadwa anali Merabu,+ ndipo wamng’ono anali Mikala.+

  • 1 Samueli 18:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ndiyeno Sauli anauza Davide kuti: “Mwana wanga wamkazi wamkulu Merabu+ alipo. Ndidzakupatsa ameneyu kuti akhale mkazi wako.+ Koma iwe undisonyeze kulimba mtima kwako ndi kumenya nkhondo za Yehova.”+ Mumtima mwake Sauli anati: “Ndisamuphe ndine ndi dzanja langa, koma amuphe ndi Afilisiti.”+

  • 1 Samueli 18:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Chotero Sauli anati: “Ndidzam’patsa Mikala kuti akhale msampha kwa iye,+ ndi kuti Afilisiti amuphe.” Zitatero Sauli anauza Davide kuti: “Lero uchite nane mgwirizano wa ukwati mwa kutenga mmodzi mwa akazi awiriwa.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena