1 Samueli 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno Sauli anadzisankhira amuna 3,000 a mu Isiraeli. Amuna 2,000 anali ndi Sauliyo ku Mikimasi+ ndi kudera lamapiri la Beteli. Amuna 1,000 anali ndi Yonatani+ ku Gibeya+ wa ku Benjamini, ndipo anthu ena onse otsalawo anawabweza kumahema awo. 1 Samueli 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndiyeno tsiku lina zinachitika kuti Yonatani+ mwana wa Sauli anauza mtumiki wake womunyamulira zida kuti: “Tiye tiwolokere kumudzi wa asilikali a Afilisiti umene uli patsidyapo.” Koma Yonatani sanauze bambo ake zimenezi.+ 1 Mbiri 9:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Nera+ anabereka Kisi,+ Kisi anabereka Sauli,+ Sauli anabereka Yonatani,+ Malikisuwa,+ Abinadabu,+ ndi Esibaala.+
2 Ndiyeno Sauli anadzisankhira amuna 3,000 a mu Isiraeli. Amuna 2,000 anali ndi Sauliyo ku Mikimasi+ ndi kudera lamapiri la Beteli. Amuna 1,000 anali ndi Yonatani+ ku Gibeya+ wa ku Benjamini, ndipo anthu ena onse otsalawo anawabweza kumahema awo.
14 Ndiyeno tsiku lina zinachitika kuti Yonatani+ mwana wa Sauli anauza mtumiki wake womunyamulira zida kuti: “Tiye tiwolokere kumudzi wa asilikali a Afilisiti umene uli patsidyapo.” Koma Yonatani sanauze bambo ake zimenezi.+
39 Nera+ anabereka Kisi,+ Kisi anabereka Sauli,+ Sauli anabereka Yonatani,+ Malikisuwa,+ Abinadabu,+ ndi Esibaala.+