1 Samueli 14:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Thanthwe limodzi looneka ngati dzinolo linali kumpoto ndipo linaima ngati chipilala moyang’ana ku Mikimasi,+ ndipo linalo linali kum’mwera moyang’ana ku Geba.+ Yesaya 10:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Iye waukira Ayati.+ Wadutsa ku Migironi. Waika katundu wake ku Mikimasi.+
5 Thanthwe limodzi looneka ngati dzinolo linali kumpoto ndipo linaima ngati chipilala moyang’ana ku Mikimasi,+ ndipo linalo linali kum’mwera moyang’ana ku Geba.+