1 Samueli 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno Sauli anadzisankhira amuna 3,000 a mu Isiraeli. Amuna 2,000 anali ndi Sauliyo ku Mikimasi+ ndi kudera lamapiri la Beteli. Amuna 1,000 anali ndi Yonatani+ ku Gibeya+ wa ku Benjamini, ndipo anthu ena onse otsalawo anawabweza kumahema awo. 1 Samueli 14:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Choncho pa tsiku limenelo, iwo anapitiriza kupha Afilisiti kuyambira ku Mikimasi+ mpaka ku Aijaloni,+ moti anthu anatopa kwambiri.+
2 Ndiyeno Sauli anadzisankhira amuna 3,000 a mu Isiraeli. Amuna 2,000 anali ndi Sauliyo ku Mikimasi+ ndi kudera lamapiri la Beteli. Amuna 1,000 anali ndi Yonatani+ ku Gibeya+ wa ku Benjamini, ndipo anthu ena onse otsalawo anawabweza kumahema awo.
31 Choncho pa tsiku limenelo, iwo anapitiriza kupha Afilisiti kuyambira ku Mikimasi+ mpaka ku Aijaloni,+ moti anthu anatopa kwambiri.+