1 Samueli 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno Sauli anadzisankhira amuna 3,000 a mu Isiraeli. Amuna 2,000 anali ndi Sauliyo ku Mikimasi+ ndi kudera lamapiri la Beteli. Amuna 1,000 anali ndi Yonatani+ ku Gibeya+ wa ku Benjamini, ndipo anthu ena onse otsalawo anawabweza kumahema awo.
2 Ndiyeno Sauli anadzisankhira amuna 3,000 a mu Isiraeli. Amuna 2,000 anali ndi Sauliyo ku Mikimasi+ ndi kudera lamapiri la Beteli. Amuna 1,000 anali ndi Yonatani+ ku Gibeya+ wa ku Benjamini, ndipo anthu ena onse otsalawo anawabweza kumahema awo.