1 Samueli 18:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno Davide atangomaliza kulankhula ndi Sauli, Yonatani+ anagwirizana kwambiri+ ndi Davide, moti anayamba kukonda Davide ngati mmene anali kudzikondera yekha.+ 2 Samueli 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako Davide anamufunsa kuti: “Zayenda bwanji kumeneko? Chonde, ndiuze.” Iye anayankha kuti: “Anthu athawa kunkhondo komanso anthu ambiri agwa ndipo afa,+ ngakhalenso Sauli+ ndi mwana wake Yonatani+ afa.” 2 Samueli 21:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma mfumu inamvera chisoni Mefiboseti+ mwana wamwamuna wa Yonatani, mwana wa Sauli, chifukwa cha lumbiro+ limene Davideyo ndi Yonatani mwana wa Sauli anachita pakati pawo pamaso pa Yehova.
18 Ndiyeno Davide atangomaliza kulankhula ndi Sauli, Yonatani+ anagwirizana kwambiri+ ndi Davide, moti anayamba kukonda Davide ngati mmene anali kudzikondera yekha.+
4 Kenako Davide anamufunsa kuti: “Zayenda bwanji kumeneko? Chonde, ndiuze.” Iye anayankha kuti: “Anthu athawa kunkhondo komanso anthu ambiri agwa ndipo afa,+ ngakhalenso Sauli+ ndi mwana wake Yonatani+ afa.”
7 Koma mfumu inamvera chisoni Mefiboseti+ mwana wamwamuna wa Yonatani, mwana wa Sauli, chifukwa cha lumbiro+ limene Davideyo ndi Yonatani mwana wa Sauli anachita pakati pawo pamaso pa Yehova.