1 Samueli 31:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Afilisiti anayandikira kwambiri Sauli ndi ana ake, ndipo pamapeto pake anapha Yonatani,+ Abinadabu+ ndi Malikisuwa,+ ana aamuna a Sauli. 1 Mbiri 10:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chotero Sauli ndi ana ake atatu anafa,+ ndipo anthu onse a m’nyumba yake anafera limodzi.
2 Afilisiti anayandikira kwambiri Sauli ndi ana ake, ndipo pamapeto pake anapha Yonatani,+ Abinadabu+ ndi Malikisuwa,+ ana aamuna a Sauli.