1 Samueli 12:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma mukachita zinthu zoipa mouma khosi, mudzasesedwa,+ inu pamodzi ndi mfumu yanuyo.”+ Hoseya 13:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno ndinakupatsa mfumu nditakwiya+ ndipo ndidzaichotsa nditakwiya.+