Yoswa 10:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pa tsiku limene Yehova anapereka Aamori kwa ana a Isiraeli, Yoswa analankhula ndi Yehova pamaso pa Aisiraeli kuti:“Dzuwa iwe,+ ima pamwamba pa Gibeoni,+Ndipo iwe mwezi, ima pamwamba pa chigwa cha Aijaloni.”+ Yoswa 19:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Saalabini,+ Aijaloni,+ Itila,
12 Pa tsiku limene Yehova anapereka Aamori kwa ana a Isiraeli, Yoswa analankhula ndi Yehova pamaso pa Aisiraeli kuti:“Dzuwa iwe,+ ima pamwamba pa Gibeoni,+Ndipo iwe mwezi, ima pamwamba pa chigwa cha Aijaloni.”+