Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 1:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Motero Mulungu anapanga zounikira zikuluzikulu ziwiri. Chounikira chokulirapo anachipanga kuti chilamulire usana, ndi chocheperapo kuti chilamulire usiku, komanso nyenyezi.+

  • 2 Mafumu 20:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Hezekiya anayankha kuti: “N’zosavuta kuti mthunzi upite kutsogolo masitepe 10, koma osati kubwerera m’mbuyo masitepe 10.”+

  • Salimo 135:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Chilichonse chimene Yehova anafuna kuchita anachita.+

      Anachita zimenezi kumwamba, padziko lapansi, m’nyanja ndi m’madzi onse akuya.+

  • Yesaya 38:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Ndichititsa mthunzi wa dzuwa+ umene wapita kale kutsogolo pamasitepe a Ahazi, kuti ubwerere m’mbuyo masitepe 10.”’”+ Choncho dzuwa linabwerera m’mbuyo pang’onopang’ono masitepe 10 pa masitepe pomwe linali litapita kale kutsogolo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena