Salimo 33:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kumwamba kunalengedwa ndi mawu a Yehova,+Ndipo makamu ake onse analengedwa ndi mpweya wa m’kamwa mwake.+
6 Kumwamba kunalengedwa ndi mawu a Yehova,+Ndipo makamu ake onse analengedwa ndi mpweya wa m’kamwa mwake.+