Aheberi 11:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mwa chikhulupiriro, timazindikira kuti mwa mawu a Mulungu, nthawi* zosiyanasiyana+ anaziika m’malo mwake,+ moti zimene zikuoneka zatuluka m’zinthu zosaoneka.+ 2 Petulo 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anthu amenewa, mwa kufuna kwawo amalephera kuzindikira mfundo iyi yakuti, panali kumwamba+ kuchokera kalekale, ndipo mwa mawu a Mulungu, dziko lapansi linali loumbika motsendereka pamwamba pa madzi+ ndi pakati pa madzi,+
3 Mwa chikhulupiriro, timazindikira kuti mwa mawu a Mulungu, nthawi* zosiyanasiyana+ anaziika m’malo mwake,+ moti zimene zikuoneka zatuluka m’zinthu zosaoneka.+
5 Anthu amenewa, mwa kufuna kwawo amalephera kuzindikira mfundo iyi yakuti, panali kumwamba+ kuchokera kalekale, ndipo mwa mawu a Mulungu, dziko lapansi linali loumbika motsendereka pamwamba pa madzi+ ndi pakati pa madzi,+