Aheberi 11:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chifukwa cha chikhulupiriro, timazindikira kuti mawu a Mulungu anachititsa kuti nthawi* zosiyanasiyana zikhale mʼmalo mwake, moti zinthu zooneka zakhalapo kuchokera ku zinthu zosaoneka. Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:3 Nsanja ya Olonda,1/15/1987, tsa. 11
3 Chifukwa cha chikhulupiriro, timazindikira kuti mawu a Mulungu anachititsa kuti nthawi* zosiyanasiyana zikhale mʼmalo mwake, moti zinthu zooneka zakhalapo kuchokera ku zinthu zosaoneka.