Aheberi 11:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mwa chikhulupiriro, timazindikira kuti mwa mawu a Mulungu, nthawi* zosiyanasiyana+ anaziika m’malo mwake,+ moti zimene zikuoneka zatuluka m’zinthu zosaoneka.+ Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:3 Nsanja ya Olonda,1/15/1987, tsa. 11
3 Mwa chikhulupiriro, timazindikira kuti mwa mawu a Mulungu, nthawi* zosiyanasiyana+ anaziika m’malo mwake,+ moti zimene zikuoneka zatuluka m’zinthu zosaoneka.+