Salimo 33:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kumwamba kunalengedwa ndi mawu a Yehova,+Ndipo makamu ake onse analengedwa ndi mpweya wa m’kamwa mwake.+ 2 Petulo 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anthu amenewa, mwa kufuna kwawo amalephera kuzindikira mfundo iyi yakuti, panali kumwamba+ kuchokera kalekale, ndipo mwa mawu a Mulungu, dziko lapansi linali loumbika motsendereka pamwamba pa madzi+ ndi pakati pa madzi,+
6 Kumwamba kunalengedwa ndi mawu a Yehova,+Ndipo makamu ake onse analengedwa ndi mpweya wa m’kamwa mwake.+
5 Anthu amenewa, mwa kufuna kwawo amalephera kuzindikira mfundo iyi yakuti, panali kumwamba+ kuchokera kalekale, ndipo mwa mawu a Mulungu, dziko lapansi linali loumbika motsendereka pamwamba pa madzi+ ndi pakati pa madzi,+