Yesaya 38:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndichititsa kuti mthunzi wa dzuwa umene wadutsa kale pamasitepe* a Ahazi, ubwerere mʼmbuyo masitepe 10.”’”+ Choncho dzuwa linabwerera mʼmbuyo masitepe 10 pamasitepe amene linali litadutsa kale. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 38:8 Nsanja ya Olonda,1/15/2007, tsa. 8 Yesaya 1, ptsa. 394-395
8 Ndichititsa kuti mthunzi wa dzuwa umene wadutsa kale pamasitepe* a Ahazi, ubwerere mʼmbuyo masitepe 10.”’”+ Choncho dzuwa linabwerera mʼmbuyo masitepe 10 pamasitepe amene linali litadutsa kale.