Yesaya 38:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndichititsa mthunzi wa dzuwa+ umene wapita kale kutsogolo pamasitepe a Ahazi, kuti ubwerere m’mbuyo masitepe 10.”’”+ Choncho dzuwa linabwerera m’mbuyo pang’onopang’ono masitepe 10 pa masitepe pomwe linali litapita kale kutsogolo.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 38:8 Nsanja ya Olonda,1/15/2007, tsa. 8 Yesaya 1, ptsa. 394-395
8 Ndichititsa mthunzi wa dzuwa+ umene wapita kale kutsogolo pamasitepe a Ahazi, kuti ubwerere m’mbuyo masitepe 10.”’”+ Choncho dzuwa linabwerera m’mbuyo pang’onopang’ono masitepe 10 pa masitepe pomwe linali litapita kale kutsogolo.+