Oweruza 1:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Choncho Aamori anakakamirabe kukhala m’phiri la Herese ndi m’mizinda ya Aijaloni+ ndi Saalibimu.+ Koma dzanja la nyumba ya Yosefe linakhala lamphamvu kwambiri, moti anayamba kugwiritsa ntchito yaukapolo Aamoriwo.+ 1 Mafumu 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 mwana wa Dekeri, amene ankayang’anira ku Makazi, ku Saalibimu,+ ku Beti-semesi,+ ndi ku Eloni-beti-hanani,
35 Choncho Aamori anakakamirabe kukhala m’phiri la Herese ndi m’mizinda ya Aijaloni+ ndi Saalibimu.+ Koma dzanja la nyumba ya Yosefe linakhala lamphamvu kwambiri, moti anayamba kugwiritsa ntchito yaukapolo Aamoriwo.+
9 mwana wa Dekeri, amene ankayang’anira ku Makazi, ku Saalibimu,+ ku Beti-semesi,+ ndi ku Eloni-beti-hanani,