Yoswa 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Aefuraimu analephera kupitikitsa Akanani+ amene anali kukhala ku Gezeri.+ Choncho Akananiwo akukhalabe pakati pa Aefuraimu mpaka lero,+ ndipo anayamba kuwagwiritsa ntchito yaukapolo.+ Yoswa 17:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ana a Isiraeli atakula mphamvu,+ anayamba kuwagwiritsa ntchito yaukapolo Akananiwo,+ ndipo sanathe kuwapitikitsiratu.+
10 Aefuraimu analephera kupitikitsa Akanani+ amene anali kukhala ku Gezeri.+ Choncho Akananiwo akukhalabe pakati pa Aefuraimu mpaka lero,+ ndipo anayamba kuwagwiritsa ntchito yaukapolo.+
13 Ana a Isiraeli atakula mphamvu,+ anayamba kuwagwiritsa ntchito yaukapolo Akananiwo,+ ndipo sanathe kuwapitikitsiratu.+