Oweruza 1:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiyeno zinachitika kuti Aisiraeli anakhala amphamvu,+ ndipo anayamba kugwiritsa ntchito yaukapolo Akananiwo,+ koma sanawachotseretu onse m’dzikolo.+
28 Ndiyeno zinachitika kuti Aisiraeli anakhala amphamvu,+ ndipo anayamba kugwiritsa ntchito yaukapolo Akananiwo,+ koma sanawachotseretu onse m’dzikolo.+