Deuteronomo 11:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Chotero muzisunga malamulo onse+ amene ndikukupatsani lero, kuti mukhale amphamvu ndi kuti mulowedi m’dziko limene mukuwolokerako ndi kulitenga kukhala lanu,+
8 “Chotero muzisunga malamulo onse+ amene ndikukupatsani lero, kuti mukhale amphamvu ndi kuti mulowedi m’dziko limene mukuwolokerako ndi kulitenga kukhala lanu,+