Yoswa 17:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ana a Isiraeli atakula mphamvu,+ anayamba kuwagwiritsa ntchito yaukapolo Akananiwo,+ ndipo sanathe kuwapitikitsiratu.+ 1 Mafumu 9:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 ana awo amene anatsala m’dzikomo, amene ana a Isiraeli analephera kuwawononga,+ Solomo anali kuwagwiritsa ntchito yaukapolo. Anthuwa akupitiriza kugwira ntchito yotere kufikira lero.+
13 Ana a Isiraeli atakula mphamvu,+ anayamba kuwagwiritsa ntchito yaukapolo Akananiwo,+ ndipo sanathe kuwapitikitsiratu.+
21 ana awo amene anatsala m’dzikomo, amene ana a Isiraeli analephera kuwawononga,+ Solomo anali kuwagwiritsa ntchito yaukapolo. Anthuwa akupitiriza kugwira ntchito yotere kufikira lero.+