Machitidwe 13:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Koma kuchokera pamenepo anthuwo ananena kuti akufuna mfumu.+ Chotero Mulungu anawapatsa Sauli mwana wa Kisi, munthu wa fuko la Benjamini,+ ndipo anakhala mfumu yawo kwa zaka 40.
21 Koma kuchokera pamenepo anthuwo ananena kuti akufuna mfumu.+ Chotero Mulungu anawapatsa Sauli mwana wa Kisi, munthu wa fuko la Benjamini,+ ndipo anakhala mfumu yawo kwa zaka 40.