2 Samueli 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno Abineri+ mwana wa Nera, amene anali mtsogoleri wa asilikali a Sauli, anatenga Isi-boseti+ mwana wa Sauli ndi kuwolokera naye ku Mahanaimu.+ 2 Samueli 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pamenepo Davide analamula anyamata ake ndipo anapha Rekabu ndi Bana+ ndipo anadula manja ndi mapazi awo. Kenako anawapachika+ pafupi ndi dziwe la ku Heburoni, koma anatenga mutu wa Isi-boseti ndi kuuika m’manda a Abineri ku Heburoni.+
8 Ndiyeno Abineri+ mwana wa Nera, amene anali mtsogoleri wa asilikali a Sauli, anatenga Isi-boseti+ mwana wa Sauli ndi kuwolokera naye ku Mahanaimu.+
12 Pamenepo Davide analamula anyamata ake ndipo anapha Rekabu ndi Bana+ ndipo anadula manja ndi mapazi awo. Kenako anawapachika+ pafupi ndi dziwe la ku Heburoni, koma anatenga mutu wa Isi-boseti ndi kuuika m’manda a Abineri ku Heburoni.+