2 Samueli 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pamenepo Davide analamula anyamata ake kuti aphe Rekabu ndi Bana.+ Kenako anawadula manja ndi mapazi nʼkuwapachika+ pafupi ndi dziwe la ku Heburoni. Koma anatenga mutu wa Isi-boseti nʼkuuika mʼmanda a Abineri ku Heburoni.
12 Pamenepo Davide analamula anyamata ake kuti aphe Rekabu ndi Bana.+ Kenako anawadula manja ndi mapazi nʼkuwapachika+ pafupi ndi dziwe la ku Heburoni. Koma anatenga mutu wa Isi-boseti nʼkuuika mʼmanda a Abineri ku Heburoni.