2 Samueli 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pamenepo Davide analamula anyamata ake ndipo anapha Rekabu ndi Bana+ ndipo anadula manja ndi mapazi awo. Kenako anawapachika+ pafupi ndi dziwe la ku Heburoni, koma anatenga mutu wa Isi-boseti ndi kuuika m’manda a Abineri ku Heburoni.+
12 Pamenepo Davide analamula anyamata ake ndipo anapha Rekabu ndi Bana+ ndipo anadula manja ndi mapazi awo. Kenako anawapachika+ pafupi ndi dziwe la ku Heburoni, koma anatenga mutu wa Isi-boseti ndi kuuika m’manda a Abineri ku Heburoni.+