2 Samueli 3:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Choncho Abineri anamuika m’manda ku Heburoni. Ali kumandako, mfumu inayamba kulira mokweza mawu ndipo anthu onse anayambanso kulira.+
32 Choncho Abineri anamuika m’manda ku Heburoni. Ali kumandako, mfumu inayamba kulira mokweza mawu ndipo anthu onse anayambanso kulira.+