1 Samueli 30:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamenepo Davide ndi anthu amene anali naye anayamba kulira mofuula+ mpaka kulefuka osathanso kulira. 2 Samueli 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Atatero, anayamba kulira ndi kubuma+ komanso kusala kudya+ mpaka madzulo chifukwa cha Sauli ndi Yonatani mwana wake, komanso chifukwa cha anthu a Yehova ndi anthu a nyumba ya Isiraeli,+ amene anali atakanthidwa ndi lupanga.
4 Pamenepo Davide ndi anthu amene anali naye anayamba kulira mofuula+ mpaka kulefuka osathanso kulira.
12 Atatero, anayamba kulira ndi kubuma+ komanso kusala kudya+ mpaka madzulo chifukwa cha Sauli ndi Yonatani mwana wake, komanso chifukwa cha anthu a Yehova ndi anthu a nyumba ya Isiraeli,+ amene anali atakanthidwa ndi lupanga.