Oweruza 21:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno anthuwo anapita ku Beteli+ ndi kukhala pansi kumeneko pamaso pa Mulungu woona+ mpaka madzulo. Iwo anali kulira kwambiri mofuula.+
2 Ndiyeno anthuwo anapita ku Beteli+ ndi kukhala pansi kumeneko pamaso pa Mulungu woona+ mpaka madzulo. Iwo anali kulira kwambiri mofuula.+