1 Samueli 30:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamenepo Davide ndi anthu amene anali naye anayamba kulira mofuula+ mpaka kulefuka osathanso kulira. Mlaliki 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Nthawi yolira+ ndi nthawi yoseka.+ Nthawi yolira mofuula+ ndi nthawi yodumphadumpha mosangalala.+
4 Pamenepo Davide ndi anthu amene anali naye anayamba kulira mofuula+ mpaka kulefuka osathanso kulira.