Genesis 23:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Sara anamwalirira ku Kiriyati-ariba,+ kapena kuti ku Heburoni,+ m’dziko la Kanani.+ Pamenepo Abulahamu analowa muhema kukamulira Sara. Yeremiya 25:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 “Fuulani, ndipo lirani abusa inu!+ Gubuduzikani pafumbi+ inu anthu otchuka pakati pa gulu la nkhosa,+ chifukwa masiku a kuphedwa ndi kubalalitsidwa kwanu afika+ ndipo mudzagwa ndi kuphwanyika ngati chiwiya chosiririka!+
2 Sara anamwalirira ku Kiriyati-ariba,+ kapena kuti ku Heburoni,+ m’dziko la Kanani.+ Pamenepo Abulahamu analowa muhema kukamulira Sara.
34 “Fuulani, ndipo lirani abusa inu!+ Gubuduzikani pafumbi+ inu anthu otchuka pakati pa gulu la nkhosa,+ chifukwa masiku a kuphedwa ndi kubalalitsidwa kwanu afika+ ndipo mudzagwa ndi kuphwanyika ngati chiwiya chosiririka!+