Ezekieli 34:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “‘Koma inu nkhosa zanga, imvani zimene Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena. Iye wanena kuti: “Ine ndidzaweruza mwachilungamo pakati pa nkhosa ndi nkhosa inzake komanso pakati pa nkhosa zamphongo ndi mbuzi zamphongo.+
17 “‘Koma inu nkhosa zanga, imvani zimene Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena. Iye wanena kuti: “Ine ndidzaweruza mwachilungamo pakati pa nkhosa ndi nkhosa inzake komanso pakati pa nkhosa zamphongo ndi mbuzi zamphongo.+