Ekisodo 15:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kenako Miriamu, mneneri wamkazi, mlongo wake wa Aroni,+ anatenga maseche m’manja mwake,+ ndipo akazi ena onse anam’tsatira akuimba maseche ndi kuvina.+ 2 Samueli 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndiyeno pamene likasa la Yehova linalowa mu Mzinda wa Davide, Mikala+ mwana wamkazi wa Sauli anasuzumira pawindo kuyang’ana pansi ndipo anaona Mfumu Davide akudumphadumpha ndi kuvina mozungulira pamaso pa Yehova. Pamenepo Mikala anayamba kum’peputsa+ mumtima mwake.+
20 Kenako Miriamu, mneneri wamkazi, mlongo wake wa Aroni,+ anatenga maseche m’manja mwake,+ ndipo akazi ena onse anam’tsatira akuimba maseche ndi kuvina.+
16 Ndiyeno pamene likasa la Yehova linalowa mu Mzinda wa Davide, Mikala+ mwana wamkazi wa Sauli anasuzumira pawindo kuyang’ana pansi ndipo anaona Mfumu Davide akudumphadumpha ndi kuvina mozungulira pamaso pa Yehova. Pamenepo Mikala anayamba kum’peputsa+ mumtima mwake.+