Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 11:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Kenako Yefita anabwerera kwawo ku Mizipa.+ Atafika kumeneko anaona mwana wake wamkazi akubwera kudzam’chingamira, akuimba maseche ndi kuvina.+ Iye anali mwana yekhayo amene anali naye. Analibenso mwana wina wamwamuna kapena wamkazi.

  • 1 Samueli 18:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ndiyeno zimene zinachitika n’zakuti, pamene asilikali anali kubwerera, Davide atakantha Mfilisiti uja, akazi anayamba kutuluka m’mizinda yonse ya Isiraeli akuimba nyimbo+ ndi kuvina. Iwo anali kupita kukachingamira mfumu Sauli mosangalala,+ akuimba maseche+ komanso choimbira cha zingwe zitatu.

  • 2 Samueli 6:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Davide pamodzi ndi nyumba yonse ya Isiraeli anali kusangalala pamaso pa Yehova, akuimba mitundu yonse ya zoimbira za mtengo wofanana ndi mtengo wa mkungudza. Anali kuimbanso zeze,+ zoimbira za zingwe,+ zinganga+ ndi maseche+ osiyanasiyana.

  • Salimo 150:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Mutamandeni ndi maseche+ ndi gule wovina mozungulira.+

      Mutamandeni ndi zoimbira za zingwe+ ndi chitoliro.+

  • Yeremiya 31:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Chotero ndidzakumanganso ndipo udzakhazikika,+ iwe namwali wa Isiraeli. Udzanyamula maseche ndi kupita kukavina pamodzi ndi anthu amene akuseka.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena