Oweruza 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Patapita nthawi, ana a Amoni+ anasonkhanitsidwa pamodzi ndipo anamanga msasa wawo ku Giliyadi.+ Zitatero, ana a Isiraeli anasonkhana pamodzi ndi kumanga msasa wawo ku Mizipa.+ Oweruza 11:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pamenepo Yefita anapita ndi akulu a ku Giliyadi, ndipo anthu anamuika kukhala mtsogoleri wawo komanso mtsogoleri wa gulu lankhondo.+ Ndiyeno Yefita ananena mawu ake onse pamaso pa Yehova+ ku Mizipa.+
17 Patapita nthawi, ana a Amoni+ anasonkhanitsidwa pamodzi ndipo anamanga msasa wawo ku Giliyadi.+ Zitatero, ana a Isiraeli anasonkhana pamodzi ndi kumanga msasa wawo ku Mizipa.+
11 Pamenepo Yefita anapita ndi akulu a ku Giliyadi, ndipo anthu anamuika kukhala mtsogoleri wawo komanso mtsogoleri wa gulu lankhondo.+ Ndiyeno Yefita ananena mawu ake onse pamaso pa Yehova+ ku Mizipa.+