Genesis 19:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Nayenso mwana wamng’onoyo anabereka mwana wamwamuna, n’kumutcha dzina lakuti Beni-ami. Iye ndiye tate wa ana a Amoni+ mpaka lero. Oweruza 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kuwonjezera apo, anasonkhanitsa ana a Amoni+ ndi Amaleki+ kuti alimbane ndi Aisiraeli. Amenewa anakantha Isiraeli ndi kulanda mzinda wa mitengo ya kanjedza.+ Oweruza 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamenepo, mkwiyo wa Yehova unayakira ana a Isiraeli,+ moti anawagulitsa+ kwa Afilisiti+ ndi kwa ana a Amoni.+
38 Nayenso mwana wamng’onoyo anabereka mwana wamwamuna, n’kumutcha dzina lakuti Beni-ami. Iye ndiye tate wa ana a Amoni+ mpaka lero.
13 Kuwonjezera apo, anasonkhanitsa ana a Amoni+ ndi Amaleki+ kuti alimbane ndi Aisiraeli. Amenewa anakantha Isiraeli ndi kulanda mzinda wa mitengo ya kanjedza.+
7 Pamenepo, mkwiyo wa Yehova unayakira ana a Isiraeli,+ moti anawagulitsa+ kwa Afilisiti+ ndi kwa ana a Amoni.+