Numeri 33:56 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 56 Zikadzatero, zimene ndinafuna kuchita kwa anthuwo ndidzachita kwa inu.’”+ Oweruza 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kuwonjezera apo, anasonkhanitsa ana a Amoni+ ndi Amaleki+ kuti alimbane ndi Aisiraeli. Amenewa anakantha Isiraeli ndi kulanda mzinda wa mitengo ya kanjedza.+
13 Kuwonjezera apo, anasonkhanitsa ana a Amoni+ ndi Amaleki+ kuti alimbane ndi Aisiraeli. Amenewa anakantha Isiraeli ndi kulanda mzinda wa mitengo ya kanjedza.+