Genesis 19:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Nayenso mwana wamng’onoyo anabereka mwana wamwamuna, n’kumutcha dzina lakuti Beni-ami. Iye ndiye tate wa ana a Amoni+ mpaka lero. Oweruza 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno patapita nthawi, ana a Amoni anayamba kumenyana ndi Aisiraeli.+
38 Nayenso mwana wamng’onoyo anabereka mwana wamwamuna, n’kumutcha dzina lakuti Beni-ami. Iye ndiye tate wa ana a Amoni+ mpaka lero.