Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 2:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 ndipo uyandikire pafupi ndi ana a Amoni. Usawavutitse kapena kumenyana nawo, chifukwa sindidzakupatsa mbali iliyonse ya dziko la ana a Amoni kuti likhale lako. Dziko limeneli ndinalipereka kwa ana a Loti kuti likhale lawo.+

  • Oweruza 11:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ndiyeno patapita nthawi, ana a Amoni anayamba kumenyana ndi Aisiraeli.+

  • Nehemiya 13:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Pa tsiku limenelo buku+ la Mose linawerengedwa+ pamaso pa anthuwo. Iwo anapeza kuti m’bukumo analembamo kuti Muamoni+ ndi Mmowabu+ aliyense sayenera kubwera mumpingo wa Mulungu woona mpaka kalekale,+

  • Zefaniya 2:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli wanena kuti: “Pali ine Mulungu wamoyo,+ Mowabu adzakhala ndendende ngati Sodomu,+ ndipo ana a Amoni+ adzakhala ngati Gomora, malo odzaza zomera zoyabwa ndiponso mchere ndiponso malo abwinja mpaka kalekale.*+ Otsala mwa anthu anga adzafunkha zinthu zawo, ndipo otsala a mtundu wa anthu anga adzawagwira ukapolo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena