Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 14:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Komanso, pali ine Mulungu wamoyo, dziko lonse lapansi lidzadzaza ndi ulemerero wa Yehova.+

  • Yesaya 49:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Takweza maso ako uone zonse zimene zikuchitika mokuzungulira. Onse asonkhanitsidwa pamodzi.+ Abwera kwa iwe. Yehova wanena kuti: “Pali ine Mulungu wamoyo,+ onsewo udzadzikongoletsa nawo ngati zokongoletsera, ndipo udzawavala ngati ndiwe mkwatibwi.+

  • Yeremiya 46:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 “‘Pali ine Mulungu wamoyo, Nebukadirezara adzabwera ndi kuonekera ngati phiri la Tabori+ pakati pa mapiri ena, ndiponso ngati phiri la Karimeli+ m’mphepete mwa nyanja,’ yatero Mfumu, imene dzina lake ndi Yehova wa makamu.+

  • Aroma 14:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Malembatu amati: “‘Pali ine Mulungu wamoyo,’ watero Yehova,+ ‘bondo lililonse lidzandigwadira ine, ndipo lilime lililonse lidzavomereza poyera kwa Mulungu.’”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena