Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 19:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Malirewo anakafika ku Tabori,+ ku Sahazuma, ndi ku Beti-semesi n’kukathera ku Yorodano. Mizinda 16 ndi midzi yake.

  • Oweruza 4:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ndiyeno iye anatumiza uthenga kwa Baraki+ mwana wa Abinowamu, yemwe anali ku Kedesi-nafitali,+ womuuza kuti: “Yehova Mulungu wa Isiraeli walamula kuti, ‘Tenga amuna 10,000 pakati pa ana a Nafitali+ ndi ana a Zebuloni+ ndipo mukasonkhane paphiri la Tabori.+

  • Salimo 89:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Munapanga kumpoto ndi kum’mwera.+

      Mapiri a Tabori+ ndi Herimoni+ amafuula mokondwera ndi kutamanda dzina lanu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena