Yoswa 19:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Malirewo anakafikanso ku Tabori,+ ku Sahazuma ndi ku Beti-semesi nʼkukathera ku Yorodano. Mizinda 16 ndi midzi yake.
22 Malirewo anakafikanso ku Tabori,+ ku Sahazuma ndi ku Beti-semesi nʼkukathera ku Yorodano. Mizinda 16 ndi midzi yake.