Yoswa 19:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Malirewo anakafika ku Tabori,+ ku Sahazuma, ndi ku Beti-semesi n’kukathera ku Yorodano. Mizinda 16 ndi midzi yake.
22 Malirewo anakafika ku Tabori,+ ku Sahazuma, ndi ku Beti-semesi n’kukathera ku Yorodano. Mizinda 16 ndi midzi yake.