Genesis 30:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndiyeno Leya anati: “Mulungu wandipatsadi mphoto yabwino. Tsopano mwamuna wanga ayamba kukondwera nane,+ chifukwa ndam’berekera ana aamuna 6.”+ Chotero Leya anatcha mwanayo dzina lakuti Zebuloni.*+ Genesis 35:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ana aamuna amene Leya anaberekera Yakobo anali Rubeni+ mwana wake woyamba, Simiyoni, Levi, Yuda, Isakara ndi Zebuloni. Yoswa 19:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Maere achitatu+ anagwera ana a Zebuloni+ potsata mabanja awo. Malire a cholowa chawo anayambira ku Saridi
20 Ndiyeno Leya anati: “Mulungu wandipatsadi mphoto yabwino. Tsopano mwamuna wanga ayamba kukondwera nane,+ chifukwa ndam’berekera ana aamuna 6.”+ Chotero Leya anatcha mwanayo dzina lakuti Zebuloni.*+
23 Ana aamuna amene Leya anaberekera Yakobo anali Rubeni+ mwana wake woyamba, Simiyoni, Levi, Yuda, Isakara ndi Zebuloni.
10 Maere achitatu+ anagwera ana a Zebuloni+ potsata mabanja awo. Malire a cholowa chawo anayambira ku Saridi