Genesis 46:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ana a Zebuloni+ anali Seredi, Eloni ndi Yahaleeli.+ Genesis 49:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Zebuloni adzakhala kugombe la nyanja,+ pafupi ndi gombe lokochezapo zombo.+ Malire ake akutali adzakhala cha ku Sidoni.+ Deuteronomo 33:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kwa Zebuloni anati:+“Kondwera Zebuloni iwe, pa maulendo ako,+Ndiponso iwe Isakara, m’mahema ako.+ Chivumbulutso 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mu fuko la Zebuloni,+ 12,000.Mu fuko la Yosefe,+ 12,000.Ndipo mu fuko la Benjamini,+ anadindamo anthu 12,000.+
13 “Zebuloni adzakhala kugombe la nyanja,+ pafupi ndi gombe lokochezapo zombo.+ Malire ake akutali adzakhala cha ku Sidoni.+
8 Mu fuko la Zebuloni,+ 12,000.Mu fuko la Yosefe,+ 12,000.Ndipo mu fuko la Benjamini,+ anadindamo anthu 12,000.+