Genesis 49:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Zebuloni adzakhala kugombe la nyanja,+ pafupi ndi gombe lokochezapo zombo.+ Malire ake akutali adzakhala cha ku Sidoni.+ Deuteronomo 33:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kwa Zebuloni anati:+“Kondwera Zebuloni iwe, pa maulendo ako,+Ndiponso iwe Isakara, m’mahema ako.+
13 “Zebuloni adzakhala kugombe la nyanja,+ pafupi ndi gombe lokochezapo zombo.+ Malire ake akutali adzakhala cha ku Sidoni.+