Salimo 89:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Munapanga kumpoto ndi kumʼmwera.Mapiri a Tabori+ ndi Herimoni+ amatamanda dzina lanu mosangalala.