Yoswa 19:22, 23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Malirewo anakafikanso ku Tabori,+ ku Sahazuma ndi ku Beti-semesi nʼkukathera ku Yorodano. Mizinda 16 ndi midzi yake. 23 Ichi chinali cholowa cha fuko la Isakara motsatira mabanja awo,+ ndipo imeneyi inali mizinda yawo ndi midzi yake.
22 Malirewo anakafikanso ku Tabori,+ ku Sahazuma ndi ku Beti-semesi nʼkukathera ku Yorodano. Mizinda 16 ndi midzi yake. 23 Ichi chinali cholowa cha fuko la Isakara motsatira mabanja awo,+ ndipo imeneyi inali mizinda yawo ndi midzi yake.